Simon Chimbetu and Orchestra Dendera Kings – Chautah Lyrics

Chautah Lyrics

Chautah woo!
Tsiku loyamba lomwelija, lomwelija
Limene munali kulenga ine
Ndilomwelo, ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope

Chautah woo!
Tsiku loyamba lomwelija, lomwelija
Limene munali kulenga ine
Ndilomwelo, ndilomweli ndikuti beta munanchinja nkhope

Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliulira
Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliupita or bwera
Silidziwika bwino
Koma munakanchinja nkhope
Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliulira
Nkhope yanga, ndikhala ngati ndiliupita or bwera
Silidziwika bwino
Koma munakanchinja nkhope

Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa)
Oyang'ana (andiyesa wakuba ine)
Oyang'ana (andiyesa wolodza)
Chautah munakanchinja nkhope

Oyang'ana (andiyesa Chitsilu yawa)
Oyang'ana (andiyesa wakuba ine)
Oyang'ana (andiyesa wolodza)
Chautah ndaona vhuto

Dendera Kings

Yes!

Dendera Kings

Lyrics sourced via LRCLIB, contributed by its community.