Alick Macheso – Mundikumbuke Lyrics
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke amayo ndatsala ndeka ine
Mundikumbuke Amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke Amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke Amayo ndatsala ndeka
Mundikumbuke Amayo ndatsala ndeka
Amai asanafe anasiya mawu
Amai asanafe anasiya mawu oooohh
Udzafune fune moenda, bambo ulinawo
Udzafune fune moenda, bambo ulinawo
Udzafune fune moenda, bambo ulinawo
Udzafune fune moenda, bambo ulinawo
Ndili mwana wapancili, wokula NaAmai
Ndili mwana wapancili ine, wokula naAmai
Ndili wamasiye
Wokulila muumpawi
Ndili wamasiye wokulila muumpawi
Ndili wamasiye ine wokulila muumpawi
Ndili wamasiye ine wokulila muumpawi
Azimai ancili ana
Amasiye mvelani
Azimai ancili eh ana amasiye
Angazopeni monga ana anunso
Angazopeni monga ana anunso wosataya
Angazopeni ye monga ana anunso
Angazopeni ye monga ana anunso
Chifundo, ndili chifundo ine
Chifundo, ndili chifundo ine
Mavhuto, ndili mavhuto ine
Mavhuto, ndili mavhuto ine
Amai anandilela anamwalila kale
Amai anandilela ine anamwalila kale
Poenda ndimangolila,
Kukumbuka ondibala
Poenda ndimangolila ine, kukumbuka ondibala
Pogona ndimisozi chabe, bambo anga muli kuti inu
Pogona ndimisozi chabe, bambo anga muli kuti inu
Ndakulila muumpawi, wopatsa chisoni ndithu
Ndakulila muumpawi, wopatsa chisoni ndithu
Ngati muli ndiumoyo, kapena munamwalila
Ngati muli ndiumoyo, kapena munamwalila
Bwanji osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko
Bwanji osabwela kutulo, kapena ndingakondeleko
Chifundo, ndili chifundo ine
Chifundo, ndili chifundo ine
Mavhuto, ndili mavhuto ine
Mavhuto, ndili mavhuto ine